Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Magulu a mbadwa za ana a Aroni anali awa: Ana a Aroni anali Nadabu, Abihu,+ Eliezara ndi Itamara.+

  • 1 Mbiri 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Umu ndi mmene ankachitira utumiki wawo+ akalowa mʼnyumba ya Yehova mogwirizana ndi dongosolo limene Aroni kholo lawo anakhazikitsa ngati mmene Yehova Mulungu wa Isiraeli anamulamulira.

  • 2 Mbiri 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kuwonjezera pamenepo, Solomo anasankha magulu a ansembe+ kuti azitumikira mogwirizana ndi lamulo la Davide bambo ake. Anasankhanso Alevi kuti azikhala pamalo awo a ntchito nʼkumatamanda+ ndi kutumikira pamaso pa ansembe mogwirizana ndi dongosolo la tsiku ndi tsiku. Komanso anasankha alonda apageti mʼmagulu awo kuti akhale mʼmageti osiyanasiyana+ chifukwa limeneli linali lamulo la Davide munthu wa Mulungu woona.

  • 2 Mbiri 31:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Hezekiya anasankha ansembe mogwirizana ndi magulu awo+ komanso Alevi mogwirizana ndi magulu awo.+ Gulu lililonse la ansembe ndiponso la Alevi analiika mogwirizana ndi utumiki wawo+ wokhudza nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Anawasankha kuti azitumikira Mulungu, kumuyamika ndiponso kumutamanda mʼmageti a kachisi wa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena