Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pamene Yesu ankachoka kukachisi, ophunzira ake anabwera kwa iye kuti amuonetse nyumba zapakachisipo. 2 Koma iye anawauza kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+

  • Maliko 13:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yesu akutuluka mʼkachisi, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Mphunzitsi, taonani mmene miyala ndi nyumbazi zikukongolera!”+ 2 Koma Yesu anamuuza kuti: “Kodi waziona nyumba zapamwamba zimenezi? Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena