Yesaya 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Limbikitsani anthu anga. Ndithu alimbikitseni,” akutero Mulungu wanu.+ Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+
13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+