-
1 Mafumu 19:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Patapita kanthawi, mngelo wa Yehova uja anabweranso nʼkumukhudza ndipo anamuuza kuti: “Dzuka udye, popeza ulendowu ukhala wautali.”
-
-
Danieli 10:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno wooneka ngati munthu uja anandikhudzanso nʼkundipatsa mphamvu.+ 19 Kenako anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,*+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu limba mtima.” Akulankhula nane, ndinalimbikitsidwa ndipo ndinanena kuti: “Lankhulani mbuyanga chifukwa inu mwandilimbikitsa.”
-