Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera. Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.
27 Moyo wanga ukuvutika tsopano,+ kodi ndinene chiyani? Atate ndipulumutseni ku nthawi yovutayi.+ Komabe nthawi imeneyi ikuyenera kundifikira pakuti nʼchifukwa chake ndinabwera.
7 Pamene Khristu anali padzikoli,* anapereka mapemphero ochonderera ndiponso opempha, kwa amene akanatha kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula komanso akugwetsa misozi,+ ndipo anamumvera chifukwa ankaopa Mulungu.