-
Mateyu 26:65Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
65 Kenako mkulu wa ansembe anangʼamba malaya ake akunja nʼkunena kuti: “Wanyoza Mulungu! Nanga tingafunenso mboni zina pamenepa? Pano mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.
-