Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritse mawu amene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”*+ Luka 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Elizabeti ali woyembekezera kwa miyezi 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa ku Galileya, wotchedwa Nazareti.
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritse mawu amene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”*+
26 Elizabeti ali woyembekezera kwa miyezi 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa ku Galileya, wotchedwa Nazareti.