Afilipi 2:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khalani ndi maganizo amenenso Khristu Yesu anali nawo.+ 6 Ngakhale kuti iye ankaoneka ngati Mulungu,+ sanaganizirepo zoti ayese kulanda udindo wa Mulungu kuti akhale wofanana naye.+
5 Khalani ndi maganizo amenenso Khristu Yesu anali nawo.+ 6 Ngakhale kuti iye ankaoneka ngati Mulungu,+ sanaganizirepo zoti ayese kulanda udindo wa Mulungu kuti akhale wofanana naye.+