Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawauza kuti: “Chakudya changa ndi kuchita zofuna za amene anandituma+ ndi kumaliza ntchito yake.+ Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinabwera kuchokera kumwamba+ kudzachita zofuna za amene anandituma, osati zofuna zanga.+
39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
34 Yesu anawauza kuti: “Chakudya changa ndi kuchita zofuna za amene anandituma+ ndi kumaliza ntchito yake.+
38 Chifukwa ndinabwera kuchokera kumwamba+ kudzachita zofuna za amene anandituma, osati zofuna zanga.+