Machitidwe 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iwo anati: “Khulupirira Ambuye Yesu ndipo udzapulumuka limodzi ndi anthu a mʼnyumba yako.”+ 1 Yohane 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Lamulo limene anatipatsa ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro mʼdzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.
23 Lamulo limene anatipatsa ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro mʼdzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.