Salimo 78:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.Anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Ankawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+