Yohane 10:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nkhosa zanga zimamva mawu anga. Ine ndimazidziwa ndipo nkhosazo zimanditsatira.+ 28 Ndidzazipatsa moyo wosatha+ ndipo sizidzawonongeka komanso palibe amene adzazitsomphole mʼdzanja langa.+
27 Nkhosa zanga zimamva mawu anga. Ine ndimazidziwa ndipo nkhosazo zimanditsatira.+ 28 Ndidzazipatsa moyo wosatha+ ndipo sizidzawonongeka komanso palibe amene adzazitsomphole mʼdzanja langa.+