Luka 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kutacha, anaitana ophunzira ake nʼkusankhapo 12, amenenso anawapatsa dzina lakuti atumwi.+