Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+ Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+
47 Ndipo tsiku ndi tsiku iye anapitiriza kuphunzitsa mʼkachisimo. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu ankafunitsitsa kumupha.+