Yohane 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mudzandifunafuna koma simudzandipeza, ndipo kumene ndidzapiteko inu simudzatha kukafikako.”+ Yohane 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anzanga apamtima inu,* ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo mogwirizana ndi zimene ndinauza Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo.
33 Anzanga apamtima inu,* ndikhala nanu kanthawi kochepa chabe. Mudzandifunafuna, ndipo mogwirizana ndi zimene ndinauza Ayuda aja kuti, ‘Kumene ine ndikupita simungathe kukafikako,’+ tsopano ndikuuzanso inuyo.