2 Ana anga okondedwa, ndikukulemberani zinthu izi kuti musachite tchimo. Komabe, wina akachita tchimo, tili ndi wotithandiza wolungama,+ Yesu Khristu,+ amene ali ndi Atate. 2 Iye anakhala nsembe yophimba+ machimo athu.+ Osati athu okha, komanso a dziko lonse lapansi.+