Mateyu 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha usiku uno, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa ndipo nkhosa zamʼgululo zidzabalalika.’+ Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+ Yohane 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine mʼbusa wabwino.+ Mʼbusa wabwino amapereka moyo wake chifukwa cha nkhosa.+
31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha usiku uno, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa ndipo nkhosa zamʼgululo zidzabalalika.’+
27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+