Yohane 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (Yohane ankachitira umboni za iye, moti ankachita kufuula kuti: “Uyu ndi amene ndinkanena uja kuti, ‘Amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndi wamkulu kuposa ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.’”)+
15 (Yohane ankachitira umboni za iye, moti ankachita kufuula kuti: “Uyu ndi amene ndinkanena uja kuti, ‘Amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndi wamkulu kuposa ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.’”)+