Yohane 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tiyenera kugwira ntchito za Mulungu amene anandituma kudakali masana.+ Usiku ukubwera pamene munthu sangagwire ntchito. Yohane 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+
4 Tiyenera kugwira ntchito za Mulungu amene anandituma kudakali masana.+ Usiku ukubwera pamene munthu sangagwire ntchito.
35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+