Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno ali mu Yerusalemu pachikondwerero cha Pasika, anthu ambiri anamukhulupirira* ataona zizindikiro zimene ankachita.

  • Yohane 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Choncho anthu ambiri kumeneko anamukhulupirira.

  • Yohane 12:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ansembe aakulu anapangana zoti aphenso Lazaro, 11 chifukwa Ayuda ambiri ankapita kumeneko ndi kukhulupirira Yesu chifukwa cha Lazaroyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena