Mateyu 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawiyi, ansembe aakulu ndiponso akulu anasonkhana mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembe dzina lake Kayafa.+ Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+ Machitidwe 4:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsiku lotsatira, olamulira ndi akulu ndiponso alembi anasonkhana ku Yerusalemu. 6 Panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda ndiponso anthu onse omwe anali achibale a wansembe wamkuluyo.
3 Pa nthawiyi, ansembe aakulu ndiponso akulu anasonkhana mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembe dzina lake Kayafa.+
2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+
5 Tsiku lotsatira, olamulira ndi akulu ndiponso alembi anasonkhana ku Yerusalemu. 6 Panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda ndiponso anthu onse omwe anali achibale a wansembe wamkuluyo.