23 Patatha zaka ziwiri, antchito a Abisalomu ankameta ubweya wa nkhosa ku Baala-hazori, pafupi ndi Efuraimu.+ Ndipo Abisalomu anaitana ana onse aamuna a mfumu.+
19 Abiya anapitiriza kuthamangitsa Yerobowamu ndipo anamulanda mizinda yake. Analanda Beteli+ ndi midzi yake yozungulira, Yesana ndi midzi yake yozungulira ndiponso Efuraini+ ndi midzi yake yozungulira.