Yohane 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba nʼkunena kuti: “Atate, nthawi yafika. Lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+
17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba nʼkunena kuti: “Atate, nthawi yafika. Lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+