Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi. Yesaya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ndinamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Kodi nditumize ndani, ndipo ndi ndani amene apite mʼmalo mwa ife?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ine ndilipo! Nditumizeni.”+
6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi.
8 Kenako ndinamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Kodi nditumize ndani, ndipo ndi ndani amene apite mʼmalo mwa ife?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ine ndilipo! Nditumizeni.”+