Yohane 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pambuyo pa zinthu zimenezi, Yosefe wa ku Arimateya, amene anali wophunzira wachinsinsi wa Yesu chifukwa ankaopa Ayuda,+ anapempha Pilato kuti akachotse mtembo wa Yesu ndipo Pilato anamupatsa chilolezo. Choncho anafika nʼkuchotsa mtembowo.+
38 Pambuyo pa zinthu zimenezi, Yosefe wa ku Arimateya, amene anali wophunzira wachinsinsi wa Yesu chifukwa ankaopa Ayuda,+ anapempha Pilato kuti akachotse mtembo wa Yesu ndipo Pilato anamupatsa chilolezo. Choncho anafika nʼkuchotsa mtembowo.+