Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuwala kwafika mʼdziko+ koma mʼmalo mokonda kuwala anthu akukonda mdima popeza ntchito zawo nʼzoipa, nʼchifukwa chake adzaweruzidwe. Yohane 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 12 Kenako Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala kwa dziko.+ Aliyense wonditsatira ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala ndi kuwala+ kwa moyo.” Yohane 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene ine ndili mʼdziko, ndine kuwala kwa dzikoli.”+
19 Kuwala kwafika mʼdziko+ koma mʼmalo mokonda kuwala anthu akukonda mdima popeza ntchito zawo nʼzoipa, nʼchifukwa chake adzaweruzidwe.
8 12 Kenako Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala kwa dziko.+ Aliyense wonditsatira ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala ndi kuwala+ kwa moyo.”