Yohane 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ine ndimalankhula zimene ndinaziona pamene ndinali ndi Atate wanga,+ koma inu mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.” Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.
38 Ine ndimalankhula zimene ndinaziona pamene ndinali ndi Atate wanga,+ koma inu mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.”
10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.