Afilipi 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khalani ndi maganizo amenenso Khristu Yesu anali nawo.+ 1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+ 1 Yohane 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu amene amanena kuti ndi wogwirizana naye, ayenera kupitiriza kuyenda mmene iyeyo ankayendera.+
21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
6 Munthu amene amanena kuti ndi wogwirizana naye, ayenera kupitiriza kuyenda mmene iyeyo ankayendera.+