Mateyu 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+ Maliko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+ Luka 22:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sukundidziwa.”+ Yohane 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Petulo anakananso ndipo nthawi yomweyo tambala analira.+
34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+
30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+
34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sukundidziwa.”+