-
Aefeso 4:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yesu ankaphunzitsa choonadi, moti ngati munamva zimene ankaphunzitsa ndiponso munaphunzitsidwa ndi iye, ndiye kuti zinthu zimenezo mukuzidziwa bwino.
-