1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.