Yohane 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+ Yohane 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomaliza adzapereka umboni wonena za chiweruzo, chifukwa wolamulira wa dziko lino waweruzidwa.+