Yohane 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa ankaopa atsogoleri achipembedzo a Chiyuda.+ Chifukwa iwo anali atagwirizana kale kuti ngati wina angavomereze kuti Yesu ndi Khristu, azimuchotsa musunagoge.+
22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa ankaopa atsogoleri achipembedzo a Chiyuda.+ Chifukwa iwo anali atagwirizana kale kuti ngati wina angavomereze kuti Yesu ndi Khristu, azimuchotsa musunagoge.+