Yohane 5:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso Atate amene anandituma andichitira umboni.+ Inu simunamvepo mawu ake nthawi ina iliyonse kapena kuona thupi lake.+ 38 Mawu akenso sanakhazikike mwa inu, chifukwa simunakhulupirire amene Atatewo anamutumiza.
37 Komanso Atate amene anandituma andichitira umboni.+ Inu simunamvepo mawu ake nthawi ina iliyonse kapena kuona thupi lake.+ 38 Mawu akenso sanakhazikike mwa inu, chifukwa simunakhulupirire amene Atatewo anamutumiza.