-
Machitidwe 21:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma titakhala masiku ndithu, mneneri wina dzina lake Agabo+ anabwera kuchokera ku Yudeya. 11 Iye anafika kwa ife nʼkutenga lamba wa Paulo. Kenako anadzimanga mapazi ndi manja nʼkunena kuti: “Mzimu woyera wati, ‘Mwiniwake wa lambayu, Ayuda adzamumanga chonchi ku Yerusalemu+ nʼkumupereka kwa anthu a mitundu ina.’”+
-