1 Yohane 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti tidziwe ngati mawu ouziridwa ndi ochokera kwa Mulungu, timadziwira izi: Mawu alionse ouziridwa amene amavomereza zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu ndi ochokera kwa Mulungu.+
2 Kuti tidziwe ngati mawu ouziridwa ndi ochokera kwa Mulungu, timadziwira izi: Mawu alionse ouziridwa amene amavomereza zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu ndi ochokera kwa Mulungu.+