Yohane 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zinthu zonse zimene ine ndili nazo ndi zanu ndipo zinthu zanu zonse ndi zanga.+ Ine ndalemekezeka pakati pa anthu amene mwandipatsa.
10 Zinthu zonse zimene ine ndili nazo ndi zanu ndipo zinthu zanu zonse ndi zanga.+ Ine ndalemekezeka pakati pa anthu amene mwandipatsa.