Luka 24:51, 52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamene ankawadalitsa, analekana nawo ndipo Mulungu anamutenga kupita naye kumwamba.+ 52 Iwo anamugwadira* nʼkubwerera ku Yerusalemu akusangalala kwambiri.+
51 Pamene ankawadalitsa, analekana nawo ndipo Mulungu anamutenga kupita naye kumwamba.+ 52 Iwo anamugwadira* nʼkubwerera ku Yerusalemu akusangalala kwambiri.+