Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.” Mateyu 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha usiku uno, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa ndipo nkhosa zamʼgululo zidzabalalika.’+ Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+
7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.”
31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha usiku uno, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa ndipo nkhosa zamʼgululo zidzabalalika.’+
27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+