Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawauza kuti: “Chakudya changa ndi kuchita zofuna za amene anandituma+ ndi kumaliza ntchito yake.+
34 Yesu anawauza kuti: “Chakudya changa ndi kuchita zofuna za amene anandituma+ ndi kumaliza ntchito yake.+