Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa,*+ koma mutiteteze kwa woipayo.’+

  • 2 Atesalonika 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Ambuye ndi wokhulupirika ndipo adzakulimbitsani ndi kukutetezani kwa woipayo.

  • 1 Yohane 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tikudziwa kuti munthu aliyense yemwe ndi mwana wa Mulungu alibe chizolowezi chochita tchimo, koma mwana* wa Mulungu amamuyangʼanira ndipo woipayo sangamugwire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena