38 Koma ngati ndikuzichita, ngakhale simukundikhulupirira, khulupirirani ntchitozo,+ kuti mudziwe ndi kupitirizabe kudziwa kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana.”+
10 Kodi sukukhulupirira kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ndimakuuzani sindilankhula zamʼmaganizo mwanga,+ koma Atate amene ndi wogwirizana ndi ine ndi amene akuchita ntchito zake kudzera mwa ine.