2 Samueli 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu onse amʼdzikoli ankalira mokweza mawu, pamene anthu onse amene anali ndi Davide ankadutsa. Mfumu inali itaimirira pafupi ndi chigwa cha Kidironi+ ndipo anthu onse ankawoloka kulowera kumsewu wopita kuchipululu.
23 Anthu onse amʼdzikoli ankalira mokweza mawu, pamene anthu onse amene anali ndi Davide ankadutsa. Mfumu inali itaimirira pafupi ndi chigwa cha Kidironi+ ndipo anthu onse ankawoloka kulowera kumsewu wopita kuchipululu.