58 Koma Petulo anapitiriza kumutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkati, anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo kuti aone zotsatira zake.+
54 Koma Petulo ankamutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Petuloyo anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo nʼkumawotha moto walawilawi.+