Numeri 35:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamalandire dipo lowombolera moyo wa munthu amene wapha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa. Aphedwe ndithu ameneyo.+ Luka 23:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma gulu lonse linafuula kuti: “Ameneyu muthane naye basi, koma ife mutimasulire Baraba!”+ 19 (Munthu ameneyu anaponyedwa mʼndende chifukwa cha kuukira boma kumene kunachitika mumzindawo komanso chifukwa chopha munthu.) Machitidwe 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo, ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wopha anthu.+
31 Musamalandire dipo lowombolera moyo wa munthu amene wapha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa. Aphedwe ndithu ameneyo.+
18 Koma gulu lonse linafuula kuti: “Ameneyu muthane naye basi, koma ife mutimasulire Baraba!”+ 19 (Munthu ameneyu anaponyedwa mʼndende chifukwa cha kuukira boma kumene kunachitika mumzindawo komanso chifukwa chopha munthu.)
14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo, ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wopha anthu.+