Yohane 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, komanso chifukwa choti mwakhulupirira, mukhale ndi moyo mʼdzina lake.+ Yohane 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wophunzira ameneyu+ ndi amene akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.
31 Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, komanso chifukwa choti mwakhulupirira, mukhale ndi moyo mʼdzina lake.+
24 Wophunzira ameneyu+ ndi amene akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.