-
Machitidwe 10:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Ndipo okhulupirira amene anabwera ndi Petulo aja, amenenso anali odulidwa, anadabwa kwambiri. Iwo anadabwa chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inaperekedwanso kwa anthu a mitundu ina.
-