Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 6:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Chifukwa ndinabwera kuchokera kumwamba+ kudzachita zofuna za amene anandituma, osati zofuna zanga.+

  • Yohane 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iye anapitiriza kuwauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano koma ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera mʼdziko lino koma ine si wochokera mʼdziko lino.

  • Yohane 8:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Yesu anawauza kuti: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ chifukwa ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano. Sindinabwere mwakufuna kwanga koma Iyeyo ndi amene anandituma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena