-
Yohane 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anabwera kudziko lakwawo, koma anthu akwawo enieniwo sanamulandire.
-
-
Yohane 3:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndithudi ndikukuuza, zimene ife tikudziwa timazilankhula, ndipo zimene taona timazichitira umboni. Koma inu simulandira umboni umene timapereka.
-