Machitidwe 7:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma iye, atadzazidwa ndi mzimu woyera, anayangʼanitsitsa kumwamba ndipo anaona ulemerero wa Mulungu ndiponso Yesu ataima kudzanja lamanja la Mulungu.+
55 Koma iye, atadzazidwa ndi mzimu woyera, anayangʼanitsitsa kumwamba ndipo anaona ulemerero wa Mulungu ndiponso Yesu ataima kudzanja lamanja la Mulungu.+